Numeri 31:48 - Buku Lopatulika48 Pamenepo akazembe a pa ankhondo zikwi, atsogoleri a zikwi, ndi atsogoleri a mazana, anayandikiza kwa Mose; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201448 Pamenepo akazembe a pa ankhondo zikwi, atsogoleri a zikwi, ndi atsogoleri a mazana, anayandikiza kwa Mose; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa48 Pamenepo akulu a nkhondo amene ankayang'anira ankhondo onse, ndiye kuti atsogoleri olamulira ankhondo zikwi, ndi atsogoleri olamulira ankhondo mazana, adabwera kwa Mose. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero48 Pamenepo omwe ankayangʼanira magulu a ankhondo olamulira 1,000 ndi olamulira 100 anabwera kwa Mose, Onani mutuwo |