Numeri 31:38 - Buku Lopatulika38 Ndipo ng'ombe zidafikira zikwi makumi atatu mphambu zisanu ndi chimodzi; pamenepo msonkho wa Yehova ndiwo makumi asanu ndi awiri mphambu ziwiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201438 Ndipo ng'ombe zidafikira zikwi makumi atatu mphambu zisanu ndi chimodzi; pamenepo msonkho wa Yehova ndiwo makumi asanu ndi awiri mphambu ziwiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa38 Ng'ombe zinalipo 36,000, ndipo 72 zinali gawo la Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero38 ngʼombe zinalipo 36,000 ndipo gawo la Yehova linali 72; Onani mutuwo |