Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 29:37 - Buku Lopatulika

37 nsembe yake yaufa, ndi nsembe zake zothira za ng'ombe, za nkhosa zamphongo, ndi za anaankhosa, monga mwa kuwerenga kwake, ndi kutsata lemba lake;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

37 nsembe yake yaufa, ndi nsembe zake zothira za ng'ombe, za nkhosa zamphongo, ndi za anaankhosa, monga mwa kuwerenga kwake, ndi kutsata lemba lake;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

37 Ndipo mupereke chopereka chake cha chakudya ndi chakumwa pa ng'ombe yamphongo ija, pa nkhosa yamphongo ija, ndi pa anaankhosa aja, molingana ndi chiŵerengero cha nyamazo ndi potsata malangizo ake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

37 Pamodzi ndi ngʼombe yayimunayo, nkhosa yayimunayo ndi ana ankhosawo, muzipereka chopereka cha chakudya ndi chakumwa molingana ndi chiwerengero cha nyamazo.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 29:37
2 Mawu Ofanana  

koma mubwere nayo nsembe yopsereza ndiyo nsembe yamoto, ya fungo lokoma kwa Yehova: ng'ombe imodzi, nkhosa yamphongo imodzi, anaankhosa asanu ndi awiri, a chaka chimodzi, opanda chilema;


ndi tonde mmodzi wa nsembe yauchimo; pamodzi ndi nsembe yopsereza yosakeleza, ndi nsembe yake yaufa, ndi nsembe yake yothira.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa