Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Nehemiya 9:36 - Buku Lopatulika

36 Tapenyani, ife lero ndife akapolo, ndi dzikoli mudalipereka kwa makolo athu kudya zipatso zake ndi zokoma zake, taonani, ife ndife akapolo m'menemo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

36 Tapenyani, ife lero ndife akapolo, ndi dzikoli mudalipereka kwa makolo athu kudya zipatso zake ndi zokoma zake, taonani, ife ndife akapolo m'menemo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

36 Onani, ife ndife akapolo lero lino, ndife akapolo m'dziko limene mudapatsa makolo athu, kuti azidya zipatso zake ndi zabwino zake zonse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

36 “Tsono, taonani! Ife lero ndife akapolo, ndife akapolo mʼdziko limene munapereka kwa makolo athu kuti azidya zipatso zake ndi zabwino zake zonse.

Onani mutuwo Koperani




Nehemiya 9:36
5 Mawu Ofanana  

Koma adzakhala akapolo ake, kuti adziwe kunditumikira kwanga, ndi kuwatumikira kwa maufumu a maiko.


Popeza ife ndife akapolo, koma Mulungu wathu sanatisiye mu ukapolo wathu, natifikitsira chifundo pamaso pa mafumu a Persiya, kuti atitsitsimutse kuimika nyumba ya Mulungu wathu, ndi kukonzanso muunda wake, ndi kutipatsa linga mu Yuda ndi mu Yerusalemu.


Tinamwa madzi athu ndi ndalama, tiona nkhuni zathu pozigula.


Otilondola atigwira pakhosi pathu, tatopa osaona popumira.


chifukwa chake mudzatumikira adani anu amene Yehova adzakutumizirani, ndi njala, ndi ludzu, ndi usiwa, ndi kusowa zinthu zonse; ndipo adzaika goli lachitsulo pakhosi panu, kufikira atakuonongani.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa