Nehemiya 6:17 - Buku Lopatulika17 Masikuwo aufulu a Yuda analemberanso makalata ambiri kwa Tobiya; ndipo anawafikanso makalata ake a Tobiya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Masikuwo aufulu a Yuda analemberanso akalata ambiri kwa Tobiya; ndipo anawafikanso akalata ake a Tobiya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Kuwonjezera apo, nthaŵi imeneyo atsogoleri a ku Yuda ankalemberana makalata ndi Tobiya, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Komanso masiku amenewo anthu olemekezeka a ku Yuda ankalemberana naye makalata ambiri ndi Tobiyayo, Onani mutuwo |