Nehemiya 12:45 - Buku Lopatulika45 Ndipo iwo anasunga udikiro wa Mulungu wao, ndi udikiro wa mayeretsedwe; momwemonso oimbira ndi odikira, monga mwa lamulo la Davide ndi la Solomoni mwana wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201445 Ndipo iwo anasunga udikiro wa Mulungu wao, ndi udikiro wa mayeretsedwe; momwemonso oimbira ndi odikira, monga mwa lamulo la Davide ndi la Solomoni mwana wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa45 chifukwa ankachita zimene Mulungu wao adaalamula, makamaka mwambo wopatulira zinthu. Oimba nyimbo ndiponso alonda a ku Nyumba ya Mulungu nawonso ankagwira ntchito zao potsata lamulo la Davide ndi Solomoni mwana wake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero45 Iwowa ankagwira ntchito ya Mulungu wawo, makamaka mwambo woyeretsa zinthu. Nawonso oyimba nyimbo ndi olonda ku Nyumba ya Mulungu anagwira ntchito zawo monga Davide ndi mwana wake Solomoni analamula. Onani mutuwo |