Nehemiya 12:42 - Buku Lopatulika42 ndi Maaseiya, ndi Semaya, ndi Eleazara, ndi Uzi, ndi Yehohanani, ndi Malikiya, ndi Elamu, ndi Ezere. Ndipo oimbira anaimbitsa Yezeraya ndiye woyang'anira wao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201442 ndi Maaseiya, ndi Semaya, ndi Eleazara, ndi Uzi, ndi Yehohanani, ndi Malikiya, ndi Elamu, ndi Ezere. Ndipo oimbira anaimbitsa Yezeraya ndiye woyang'anira wao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa42 Panalinso ansembe aŵa: Maaseiya, Semaya, Eleazara, Uzi, Yehohanani, Malikiya, Elamu ndi Ezero. Yezeraya ndiye ankatsogolera oimba nyimbo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero42 Panalinso ansembe awa: Maaseya, Semaya, Eliezara, Uzi, Yehohanani, Milikiya, Elamu ndi Ezeri. Gulu loyimba linkatsogozedwa ndi Yezirahayiya. Onani mutuwo |