Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Nehemiya 12:41 - Buku Lopatulika

41 ndi ansembe, Eliyakimu, Maaseiya, Miniyamini, Mikaya, Eliyoenai, Zekariya, ndi Hananiya, ali nao malipenga;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

41 ndi ansembe, Eliyakimu, Maaseiya, Miniyamini, Mikaya, Eliyoenai, Zekariya, ndi Hananiya, ali nao malipenga;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

41 panali ansembe aŵa akuimba malipenga: Eliyakimu, Maaseiya, Miniyamini, Mikaya, Eliyoenai, Zekariya ndi Hananiya.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

41 panalinso ansembe awa akuyimba malipenga: Eliyakimu, Maaseya, Miniyamini, Mikaya, Eliyoenai, Zekariya ndi Hananiya.

Onani mutuwo Koperani




Nehemiya 12:41
4 Mawu Ofanana  

Mesulamu, Abiya, Miyamini,


Atatero, magulu awiriwo a iwo oyamikira anaima m'nyumba ya Mulungu, ndipo ine ndi limodzi la magawo awiri a olamulira pamodzi ndi ine;


ndi Maaseiya, ndi Semaya, ndi Eleazara, ndi Uzi, ndi Yehohanani, ndi Malikiya, ndi Elamu, ndi Ezere. Ndipo oimbira anaimbitsa Yezeraya ndiye woyang'anira wao.


Ndi Yesuwa, ndi Bani, ndi Serebiya, Yamini, Akubu, Sabetai, Hodiya, Maaseiya, Kelita, Azariya, Yozabadi, Hanani, Pelaya, ndi Alevi, anadziwitsa anthu chilamulocho; ndi anthu anali chilili pamalo pao.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa