Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Nehemiya 12:40 - Buku Lopatulika

40 Atatero, magulu awiriwo a iwo oyamikira anaima m'nyumba ya Mulungu, ndipo ine ndi limodzi la magawo awiri a olamulira pamodzi ndi ine;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

40 Atatero, magulu awiriwo a iwo oyamikira anaima m'nyumba ya Mulungu, ndipo ine ndi limodzi la magawo awiri a olamulira pamodzi ndi ine;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

40 Choncho magulu othokoza aŵiri onsewo adakaimirira pafupi ndi Nyumba ya Mulungu. Pamodzi ndi ine ndi theka la akuluakulu aja,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

40 Choncho magulu onse awiri oyimba nyimbo zothokoza aja anakayima pafupi ndi Nyumba ya Mulungu. Pamodzi ndi ine ndi theka la atsogoleri aja,

Onani mutuwo Koperani




Nehemiya 12:40
7 Mawu Ofanana  

Ndipo anathirirana mang'ombe, kulemekeza ndi kuyamika Yehova, ndi kuti, Pakuti ndiye wabwino, pakuti chifundo chake nchosalekeza pa Israele. Nafuula anthu onse ndi chimfuu chachikulu, pomlemekeza Yehova; popeza adamanga maziko a nyumba ya Yehova.


ndi pamwamba pa Chipata cha Efuremu, ndi ku Chipata Chakale, ndi ku Chipata cha Nsomba, ndi Nsanja ya Hananele, ndi Nsanja ya Zana, mpaka ku Chipata cha Nkhosa; ndipo anaima ku Chipata cha Akaidi.


ndi ansembe, Eliyakimu, Maaseiya, Miniyamini, Mikaya, Eliyoenai, Zekariya, ndi Hananiya, ali nao malipenga;


Ndidzikumbukira izi ndipo nditsanulira moyo wanga m'kati mwa ine, pakuti ndinkapita ndi unyinji wa anthu, ndinawatsogolera kunyumba ya Mulungu, ndi mau akuimbitsa ndi kuyamika, ndi unyinji wakusunga dzuwa lokondwera.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa