Nehemiya 12:36 - Buku Lopatulika36 ndi abale ake: Semaya, ndi Azarele, Milalai, Gilalai, Maai, Netanele, ndi Yuda, Hanani, ndi zoimbira za Davide munthu wa Mulungu; ndi Ezara mlembiyo anawatsogolera; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 ndi abale ake: Semaya, ndi Azarele, Milalai, Gilalai, Maai, Netanele, ndi Yuda, Hanani, ndi zoimbira za Davide munthu wa Mulungu; ndi Ezara mlembiyo anawatsogolera; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 Panali achibale ao aŵa: Semaya, Azarele, Milalai, Gilalai, Maai, Netanele, Yuda, ndi Hanani. Iwowo ankanyamula zoimbira zopangidwa ndi Davide, munthu wa Mulungu uja. Mlembi Ezara ndiye ankaŵatsogolera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 pamodzi ndi abale awo awa: Semaya, Azareli, Milalai, Gilalayi, Maayi, Netaneli, Yuda ndi Hanani. Onse ankagwiritsa ntchito zida zoyimbira za Davide, munthu wa Mulungu. Tsono Ezara mlembi uja ankawatsogolera. Onani mutuwo |
Ndipo anaika monga mwa chiweruzo cha Davide atate wake zigawo za ansembe ku utumiki wao, ndi Alevi ku udikiro wao, kulemekeza Mulungu, ndi kutumikira pamaso pa ansembe, monga munayenera tsiku ndi tsiku; odikira omwe monga mwa zigawo zao ku chipata chilichonse; pakuti momwemo Davide munthu wa Mulungu adamuuza.