Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Nehemiya 12:29 - Buku Lopatulika

29 ndi ku Betegiligala, ndi ku minda ya Geba ndi Azimaveti; popeza oimbirawo adadzimangira midzi pozungulira Yerusalemu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

29 ndi ku Betegiligala, ndi ku minda ya Geba ndi Azimaveti; popeza oimbirawo adadzimangira midzi pozungulira Yerusalemu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

29 Kudabwera enanso ochokera ku Betegiligala, ku Geba, ndi ku Azimaveti, pakuti oimba nyimbo anali atamanga midzi yao pozungulira Yerusalemu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

29 Beti-Giligala ndi ku madera a ku Geba ndi Azimaveti, pakuti oyimbawo anali atamanga midzi yawo mozungulira Yerusalemu.

Onani mutuwo Koperani




Nehemiya 12:29
12 Mawu Ofanana  

ndi ku fuko la Benjamini Geba ndi mabusa ake, ndi Alemeti ndi mabusa ake, ndi Anatoti ndi mabusa ake. Mizinda yao yonse mwa mabanja ao ndiyo mizinda khumi ndi itatu.


Ana a Azimaveti, makumi anai mphambu awiri.


Ana a Benjamini omwe, kuyambira ku Geba pa Mikimasi, ndi Aya, ndi pa Betele ndi midzi yake,


Ana a oimbirawo anasonkhana ochokera ku dziko lozungulira Yerusalemu, ndi kumidzi ya Anetofa,


Ndipo ansembe ndi Alevi anadziyeretsa okha, nayeretsa anthu, ndi zipata, ndi linga.


Ndinazindikiranso kuti sanapereke kwa Alevi magawo ao; m'mwemo Alevi ndi oimbira adathawira yense kumunda wake.


Amuna a ku Betazimaveti, makumi anai kudza awiri.


Amuna a ku Rama ndi Geba, mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi awiri kudza mmodzi.


Sakhala kodi tsidya lija la Yordani, m'tseri mwake mwa njira yake yolowa dzuwa, m'dziko la Akanani, akukhala m'chidikha, pandunji pake pa Giligala, pafupi pa mathundu a More?


Pamenepo Yoswa ndi Aisraele onse naye, anabwerera kuchigono ku Giligala.


Ndipo motapira fuko la Benjamini, Gibiyoni ndi mabusa ake, Geba ndi mabusa ake,


Ndipo Yehova anati kwa Yoswa, Lero lino ndakukunkhunizirani mtonzo wa Ejipito. Chifukwa chake dzina la malowo analitcha Giligala kufikira lero lino.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa