Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Nehemiya 12:28 - Buku Lopatulika

28 Ana a oimbirawo anasonkhana ochokera ku dziko lozungulira Yerusalemu, ndi kumidzi ya Anetofa,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

28 Ana a oimbirawo anasonkhana ochokera ku dziko lozungulira Yerusalemu, ndi kumidzi ya Anetofa,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

28 Tsono anthu a m'mabanja a Levi oimba nyimbo, adasonkhana pamodzi, kuchokera ku malo onse ozungulira Yerusalemu, ndiponso ku midzi ya Anetofati.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

28 Tsono anthu a mabanja a Alevi oyimba nyimbo aja anasonkhana pamodzi kuchokera ku madera onse ozungulira Yerusalemu ndiponso ku midzi ya Anetofati,

Onani mutuwo Koperani




Nehemiya 12:28
7 Mawu Ofanana  

Ana a Salima: Betelehemu, ndi Anetofa, Ataroti-Beti-Yowabu, ndi Hazi Amanahati, ndi Azori.


ndi Obadiya mwana wa Semaya, mwana wa Galali, mwana wa Yedutuni, ndi Berekiya mwana wa Asa, mwana wa Elikana, wokhala m'midzi ya Anetofa.


ndi ku Betegiligala, ndi ku minda ya Geba ndi Azimaveti; popeza oimbirawo adadzimangira midzi pozungulira Yerusalemu.


Ndinazindikiranso kuti sanapereke kwa Alevi magawo ao; m'mwemo Alevi ndi oimbira adathawira yense kumunda wake.


Ndi potsatizana naye anakonza ansembe okhala kuchidikha.


anatumiza mau kwa ine Sanibalati ndi Gesemu, kuti, Tiyeni tikomane kumidzi ya ku Chigwa cha Ono; koma analingirira za kundichitira choipa.


Amuna a ku Betelehemu ndi ku Netofa, zana limodzi mphambu makumi asanu ndi atatu kudza asanu ndi atatu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa