Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Nehemiya 12:17 - Buku Lopatulika

17 wa Abiya, Zikiri; wa Miniyamini, wa Mowadiya, Pilitai;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 wa Abiya, Zikiri; wa Miniyamini, wa Mowadiya, Pilitai;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Wa fuko la Abiya anali Zikiri, wa fuko la Miniyamini, wa fuko la Mowadiya anali Pilitai.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 wa fuko la Abiya anali Zikiri; wa fuko la Miniyamini ndi banja la Maadiya anali Pilitayi;

Onani mutuwo Koperani




Nehemiya 12:17
7 Mawu Ofanana  

wachisanu ndi chiwiri Hakozi, wachisanu ndi chitatu Abiya,


wachisanu Malikiya, wachisanu ndi chimodzi Miyamini,


Mesulamu, Abiya, Miyamini,


wa Ido, Zekariya; wa Ginetoni, Mesulamu;


wa Biliga, Samuwa; wa Semaya, Yehonatani;


Ndi ana aamuna a Izihara ndiwo: Kora ndi Nefegi, ndi Zikiri.


Masiku a Herode, mfumu ya Yudeya, kunali munthu wansembe, dzina lake Zakariya, wa gulu la ansembe la Abiya; ndi mkazi wake wa ana aakazi a fuko la Aroni, dzina lake Elizabeti.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa