Nahumu 3:2 - Buku Lopatulika2 Kumveka kwa chikoti, ndi mkokomo wa kuyenda kwa njinga za magaleta; ndi kaphatakaphata wa akavalo, ndi gwegwegwe wa magaleta; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Kumveka kwa chikoti, ndi mkokomo wa kuyenda kwa njinga za magaleta; ndi kaphatakaphata wa akavalo, ndi gwegwegwe wa magaleta; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Imvani kulira kwa zikoti, kukokoma kwa mikombero, likitilikiti wa akavalo ndi kulilima kwa magaleta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Kulira kwa zikwapu, mkokomo wa mikombero, kufuwula kwa akavalo ndiponso phokoso la magaleta! Onani mutuwo |