Nahumu 2:6 - Buku Lopatulika6 Pa zipata za mitsinje patseguka, ndi chinyumba chasungunuka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Pa zipata za mitsinje patseguka, ndi chinyumba chasungunuka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Akutsekula zipata zotchinga dziŵe la madzi, kunyumba kwa mfumu kwadzaza mantha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Atsekula zipata zotchinga madzi a mu mtsinje ndipo nyumba yaufumu yagwa. Onani mutuwo |