Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Mlaliki 9:17 - Buku Lopatulika

17 Mau a anzeru achete amveka koposa kufuula kwa wolamulira mwa zitsiru.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 Mau a anzeru achete amveka koposa kufuula kwa wolamulira mwa zitsiru.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Mau a munthu wanzeru, olankhula mofatsa, ndi abwino kupambana kufuula kwa mfumu pa gulu la zitsiru.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 Mawu oyankhula mofatsa a munthu wanzeru, anthu amawasamalira kwambiri kupambana kufuwula kwa mfumu ya zitsiru.

Onani mutuwo Koperani




Mlaliki 9:17
10 Mawu Ofanana  

Adzamkomera mtima wodzudzula m'tsogolo mwake, koposa wosyasyalika ndi lilime lake.


Mau a m'kamwa mwa munthu wanzeru nga chisomo; koma milomo ya chitsiru idzachimeza.


Kumva chidzudzulo cha anzeru kupambana kumva nyimbo ya zitsiru.


Iye sadzafuula, ngakhale kukuwa, pena kumvetsa mau ake m'khwalala.


Iye sadzalephera kapena kudololoka, kufikira atakhazikitsa chiweruzo m'dziko lapansi; ndipo zisumbu zidzalindira chilamulo chake.


Ndipo pamene ananena izi, anamasula msonkhano.


Pakuti mkwiyo wa munthu suchita chilungamo cha Mulungu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa