Mlaliki 9:16 - Buku Lopatulika16 Pamenepo ndinati, Nzeru ipambana mphamvu; koma anyoza nzeru ya wosauka, osamvera mau ake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Pamenepo ndinati, Nzeru ipambana mphamvu; koma anyoza nzeru ya wosauka, osamvera mau ake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Ndiye ine ndikuti nzeru nzabwino ndithu kupambana mphamvu, ngakhale kuti anthu sazimvera nzeru za munthu wosauka, ndipo za mau ake salabadako nkomwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Choncho ine ndinati, “Nzeru ndi yopambana mphamvu.” Koma nzeru ya munthu wosauka imanyozedwa, ndipo palibe amene amalabadirako za mawu ake. Onani mutuwo |