Mlaliki 9:14 - Buku Lopatulika14 panali mzinda waung'ono muli anthu owerengeka; ndipo inadzako mfumu yaikulu, nawuzinga ndi nkhondo, nkumanga malinga aakulu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 panali mudzi waung'ono muli anthu owerengeka; ndipo inadzako mfumu yaikulu, niizinga ndi nkhondo, nimangapo malinga akulu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Panali mzinda waung'ono, m'mene munali anthu oŵerengeka. Tsono padafika mfumu yamphamvu kudzauthira nkhondo mzindawo, nkuuzinga ndi zithando zankhondo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Panali mzinda waungʼono umene unali ndi anthu owerengeka. Ndipo mfumu yamphamvu inabwera kudzawuthira nkhondo, inawuzungulira ndi kumanga mitumbira yankhondo. Onani mutuwo |