Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Mlaliki 7:28 - Buku Lopatulika

28 chomwe moyo wanga uchifuna chifunire, koma osachipezai ndi ichi, mwamuna mmodzi mwa chikwi ndinampezadi, koma mkazitu mwa onsewo sindinampeze.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

28 chomwe moyo wanga uchifuna chifunire, koma osachipezai ndi ichi, mwamuna mmodzi mwa chikwi ndinampezadi, koma mkazitu mwa onsewo sindinampeza.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

28 Ndizo zimene mtima wanga unkazifunafuna kaŵirikaŵiri, koma osazipeza. Ndidapeza mwamuna mmodzi yekha wolungama pakati pa anthu 1,000, koma mkazi wolungama sindidampezepo ndi mmodzi yemwe pakati pa anthu onsewo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

28 pamene ine ndinali kufufuzabe koma osapeza kanthu, ndinapeza munthu mmodzi wolungama pakati pa anthu 1,000, koma pakati pawo panalibepo mkazi mmodzi wolungama.

Onani mutuwo Koperani




Mlaliki 7:28
6 Mawu Ofanana  

Akakhala kwa iye mthenga, womasulira mau mmodzi mwa chikwi, kuonetsera munthu chomuyenera;


Pulumutsani, Yehova; pakuti wofatsa wasowa; pakuti okhulupirika achepa mwa ana a anthu.


Taonani, ichi ndachipeza, ati Mlalikiyo, m'kuphatikiza chinthu china ndi chinzake, ndikazindikire malongosoledwe ao;


Ndi moyo wanga ndinakhumba Inu usiku; inde ndi mzimu wanga wa mwa ine ndidzafuna Inu mwakhama; pakuti pamene maweruziro anu ali padziko lapansi, okhala m'dziko lapansi adzaphunzira chilungamo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa