Mlaliki 7:27 - Buku Lopatulika27 Taonani, ichi ndachipeza, ati Mlalikiyo, m'kuphatikiza chinthu china ndi chinzake, ndikazindikire malongosoledwe ao; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Taonani, ichi ndachipeza, ati Mlalikiyo, m'kuphatikiza chinthu china ndi chinzake, ndikazindikire malongosoledwe ao; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Zimenezitu nzimene ndidazipeza pakusonkhanitsa izi ndi izi, kuti ndidziŵe m'mene zinthu zimakhalira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Mlaliki akunena kuti, “Taonani, chimene ndinachipeza ndi ichi: “Kuwonjezera chinthu china pa china kuti ndidziwe mmene zinthu zimachitikira, Onani mutuwo |