Mlaliki 7:23 - Buku Lopatulika23 Ndayesa zonsezi ndi nzeru; ndinati, Ndidzakhala wanzeru; koma inanditalikira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ndayesa zonsezi ndi nzeru; ndinati, Ndidzakhala wanzeru; koma inanditalikira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Zonsezi ndidaziyesa ndi nzeru zanga. Ndinkati, “Ndidzakhala wanzeru.” Koma nzeruzo zinali nane kutali. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Zonsezi ndinaziyesa ndi nzeru zanga ndipo ndinati, “Ine ndatsimikiza mu mtima mwanga kuti ndikhale wanzeru,” koma nzeruyo inanditalikira. Onani mutuwo |