Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Mlaliki 7:19 - Buku Lopatulika

19 Nzeru ilimbitsa wanzeru koposa akulu khumi akulamulira m'mzinda.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

19 Nzeru ilimbitsa wanzeru koposa akulu khumi akulamulira m'mudzi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

19 Nzeru zimapatsa munthu mphamvu zoposa zimene angampatse atsogoleri khumi amumzinda.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

19 Nzeru zimapereka mphamvu zambiri kwa munthu wanzeru kupambana olamulira khumi a mu mzinda.

Onani mutuwo Koperani




Mlaliki 7:19
8 Mawu Ofanana  

Wanzeru akwera pa mzinda wa olimba, nagwetsa mphamvu yake imene anaikhulupirira.


Mwamuna wanzeru ngwamphamvu; munthu wodziwa ankabe nalimba.


Ndine mwini uphungu ndi kudziwitsa; ndine luntha; ndili ndi mphamvu.


Mnyamata wosauka ndi wanzeru apambana mfumu yokalamba ndi yopusa, imene sifunanso kulangidwa mwambo.


Pakuti nzeru itchinjiriza monga ndalama zitchinjiriza; koma kudziwa kupambana, chifukwa nzeru isunga moyo wa eni ake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa