Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Mlaliki 4:15 - Buku Lopatulika

15 Ndinapenyera anthu onse amoyo akuyenda kunja kuno, kuti anali ndi mwana, wachiwiri, amene adzalowa m'malo mwake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 Ndinapenyera anthu onse amoyo akuyenda kunja kuno, kuti anali ndi mwana, wachiwiri, amene adzalowa m'malo mwake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 Ndinkaganiza za anthu onse amene amakhala pansi pano, ndipo ndidazindikira kuti pakati paopo panali mnyamata uja amene anali wodzatenga malo a mfumu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 Ndipo ndinaona kuti iwo onse amene anakhala ndi moyo ndi kuyenda pansi pano anatsatira wachinyamatayo, amene anatenga malo a mfumu.

Onani mutuwo Koperani




Mlaliki 4:15
3 Mawu Ofanana  

Abisalomu anachitira zotero Aisraele onse akudza kwa mfumu kuti aweruze mlandu wao; chomwecho Abisalomu anakopa mitima ya anthu a Israele.


Pakuti atuluka m'nyumba yandende kulowa ufumu; komanso yemwe abadwa m'dziko lake asauka.


Anthu onse sawerengeka, ngakhale onsewo anawalamulira; koma amene akudza m'mbuyo sadzakondwera naye. Ichinso ndi chabe ndi chosautsa mtima.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa