Mlaliki 3:21 - Buku Lopatulika21 Ndani adziwa mzimu wa ana a anthu wokwera kumwamba, ndi mzimu wa nyama wotsikira kunsi ku dziko? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndani adziwa mzimu wa ana a anthu wokwera kumwamba, ndi mzimu wa nyama wotsikira kunsi dziko? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Kodi ndani angatsimikize kuti mzimu wa munthu ndiwo umakwera kumwamba, koma mpweya wa nyama umatsikira kunsi kwa nthaka? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Kodi ndani amene amadziwa ngati mzimu wa munthu umakwera kumwamba, ndipo mzimu wa nyama umatsikira kunsi kwa dziko?” Onani mutuwo |