Mlaliki 2:25 - Buku Lopatulika25 Pakuti ndani angadye ndi kufulumirako, koposa ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Pakuti ndani angadye ndi kufulumirako, koposa ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Nanga popanda Iye ndani angathe kudya, ndani angathe kusangalala? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 pakuti popanda Iye, ndani angadye ndi kupeza chisangalalo? Onani mutuwo |