Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Mlaliki 2:20 - Buku Lopatulika

20 Ndipo ndinatembenuka ndi kukhululuka za ntchito zanga zonse ndasauka nazo kunja kuno.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

20 Ndipo ndinatembenuka ndi kukhululuka za ntchito zanga zonse ndasauka nazo kunja kuno.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

20 Motero ndidayamba kutaya mtima chifukwa cha ntchito zonse zimene ndidazigwira movutikira pansi pano.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

20 Motero ndinayamba kutaya mtima chifukwa cha ntchito zonse zimene ndinazivutikira pansi pano.

Onani mutuwo Koperani




Mlaliki 2:20
8 Mawu Ofanana  

Mulungu Wamphamvuyonse adzakupatsani inu chifundo pamaso pa munthu uja, kuti akumasulireni inu mbale wanu wina ndi Benjamini. Ndipo ine, ngati ndikhala wopanda ana, ndikhalatu.


Ndipo ndani adziwa ngati adzakhala wanzeru pena chitsiru? Koma adzalamulira ntchito zanga zonse ndinasauka nazo, ndi kuzigwira mwanzeru kunja kuno. Ichinso ndi chabe.


Pakuti pali munthu wina agwira ntchito mwanzeru ndi modziwa nadzipinduliramo; koma adzapereka gawo lake kwa munthu amene sanagwirepo ntchito. Ichinso ndi chabe ndi choipa chachikulu.


Ngati tiyembekezera Khristu m'moyo uno wokha, tili ife aumphawi oposa a anthu onse.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa