Mlaliki 12:6 - Buku Lopatulika6 chingwe chasiliva chisanaduke, ngakhale mbale yagolide isanasweke, ngakhale mtsuko usanaphwanyike kukasupe, ngakhale njinga yotungira madzi isanathyoke kuchitsime; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 chingwe chasiliva chisanaduke, ngakhale mbale yagolide isanasweke, ngakhale mtsuko usanaphwanyike kukasupe, ngakhale njinga yotungira madzi isanathyoke kuchitsime; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Nthambo yasiliva idzamasuka, mbale yagolide idzasweka, mtsuko udzaphwanyika ku kasupe, ndipo mkombero udzathyoka ku chitsime. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Kumbukira Iye chingwe cha siliva chisanaduke, kapena mbale yagolide isanasweke; mtsuko usanasweke ku kasupe, kapena mkombero usanathyoke ku chitsime. Onani mutuwo |