Mlaliki 12:10 - Buku Lopatulika10 Mlalikiyo anasanthula akapeze mau okondweretsa, ndi zolemba zoongoka ngakhale mau oona. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Mlalikiyo anasanthula akapeze mau okondweretsa, ndi zolemba zoongoka ngakhale mau oona. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Mlalikiyo ankafunafuna mau ogwira mtima, ndipo adalemba mau oona ndi mtima wolungama. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Mlaliki anafufuzafufuza kuti apeze mawu oyenera, ndipo zimene analemba zinali zolondola ndiponso zoona. Onani mutuwo |