Mlaliki 11:10 - Buku Lopatulika10 Chifukwa chake chotsani zopweteka m'mtima mwako, nulekanitse zoipa ndi thupi lako; pakuti ubwana ndi unyamata ngwa chabe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Chifukwa chake chotsani zopweteka m'mtima mwako, nulekanitse zoipa ndi thupi lako; pakuti ubwana ndi unyamata ngwa chabe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Choncho muchotseretu zokusautsani mu mtima mwanu, mupewe zokupwetekani m'thupi mwanu. Pajatu unyamata ndi ubwana, zonse nzopandapake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Choncho uchotse zokusautsa mu mtima mwako, upewe zokupweteka mʼthupi mwako, pakuti unyamata ndi ubwana ndi zopandapake. Onani mutuwo |