Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Mlaliki 10:18 - Buku Lopatulika

18 Tsindwi litewa ndi mphwai za eni ake; nyumba nidontha ndi ulesi wa manja.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 Tsindwi litewa ndi mphwai za eni ake; nyumba nidontha ndi ulesi wa manja.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Denga limaloshoka, mwini wake akakhala waulesi, ndipo nyumba imadontha, mwiniwake akakhala nthyamba.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Ngati munthu ndi waulesi, denga lake limaloshoka; ngati manja ake ndi alobodo nyumba yake imadontha.

Onani mutuwo Koperani




Mlaliki 10:18
8 Mawu Ofanana  

Dzanja la akhama lidzalamulira; koma waulesi adzakhala ngati kapolo.


Mkazi yense wanzeru amanga banja lake; koma wopusa alipasula ndi manja ake.


Waulesi salima chifukwa cha chisanu; adzapemphapempha m'masika osalandira kanthu.


Chifuniro cha waulesi chimupha; chifukwa manja ake akana kugwira ntchito.


Pakuti wakumwaimwa ndi wosusukayo adzasauka; ndipo kusinza kudzaveka munthu nsanza.


Koma tikhumba kuti yense wa inu aonetsere changu chomwechi cholinga kuchiyembekezo chokwanira kufikira chitsiriziro;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa