Mlaliki 10:17 - Buku Lopatulika17 Mwai kwa dzikowe, pamene mfumu yako ndiye mwana wa aufulu, ndipo akalonga ako adya pa nthawi yoyenera akalimbe osati akaledzere ai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Mwai kwa dzikowe, pamene mfumu yako ndiye mwana wa aufulu, ndipo akalonga ako adya pa nthawi yoyenera akalimbe osati akaledzere ai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Koma ndiwe wodala iwe dziko, ngati mfumu yako ndi mwana wa mfulu. Ndiwe wodala ngati nduna zako zimachita phwando pa nthaŵi yabwino, kuti zikhale zamphamvu, osati kuti ziledzere. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Wodala iwe, iwe dziko ngati mfumu yako ndi mwana wolemekezeka ndipo atsogoleri ako amadya pa nthawi yake, kuti apeze mphamvu osati kuti aledzere. Onani mutuwo |