Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Mlaliki 10:15 - Buku Lopatulika

15 Ntchito ya zitsiru izitopetsa zonsezo, pakuti sichidziwa kunka kumzinda.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 Ntchito ya zitsiru izitopetsa zonsezo, pakuti sichidziwa kunka kumudzi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 Chitsiru chimagwira ntchito modzitopetsa, koma njira yopita ku mzinda sichiidziŵa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 Chitsiru chimatopa msanga ndi ntchito yochepa; ndipo sichikhala ndi mphamvu zobwererera ku mudzi.

Onani mutuwo Koperani




Mlaliki 10:15
14 Mawu Ofanana  

Anasokera m'chipululu, m'njira yopanda anthu; osapeza mzinda wokhalamo.


Ndipo anawatsogolera panjira yolunjika, kuti amuke kumzinda wokhalamo.


Chitsulo chikakhala chosathwa, ndipo ukaleka kunola, uzipambana kulimbikira; koma nzeru ipindulira pochenjeza.


Chitsiru chichulukitsanso mau; koma munthu sadziwa chimene chidzaoneka; ndipo ndani angamuuze chomwe chidzakhala m'tsogolo mwake?


Tsoka kwa dzikowe, pamene mfumu yako ndiye mwana, ndipo akalonga ako adyera mamawa!


Inde, poyendanso chitsiru panjira, nzeru yake imthera ndipo angoti kwa onse kuti, Ndine chitsiru.


Bwanji inu mulikutayira ndalama chinthu chosadya, ndi kutayira malipiro anu zosakhutitsa? Mverani Ine mosamalitsa, nimudye chimene chili chabwino, moyo wanu nukondwere ndi zonona.


Wolungama atayika, ndipo palibe munthu wosamalirapo; ndipo anthu achifundo atengedwa, palibe wolingalira kuti wolungama achotsedwa pa choipa chilinkudza.


Kodi sadzamnenera fanizo onsewo, ndi mwambi womnyodola, ndi kuti, Tsoka iye wochulukitsa zimene sizili zake? Mpaka liti? Iye wodzisenzera zigwiriro.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa