Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Miyambo 9:3 - Buku Lopatulika

3 Yatuma anamwali ake, iitana pa misanje ya m'mudzi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Yatuma anamwali ake, iitana pa misanje ya m'mudzi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Idatuma adzakazi ake kuti akakhalire pa malo apamwamba mu mzinda ndipo akalengeze kuti,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Nzeruyo inatuma adzakazi ake, kuti akakhale pamwamba penipeni pa mzinda ndi kukalengeza kuti,

Onani mutuwo Koperani




Miyambo 9:3
14 Mawu Ofanana  

Ambuye anapatsa mau, akazi akulalikira uthengawo ndiwo khamu lalikulu.


Ukhala pa khomo la nyumba yake, pampando pa misanje ya m'mudzi,


wachibwana ndani? Apatukire kuno. Ati kwa yense wopanda nzeru,


Chifukwa chake pitani inu kumphambano za njira, ndipo aliyense amene mukampeze, itanani kuukwatiku.


Mwa ichinso nzeru ya Mulungu inati, Ndidzatumiza kwa iwo aneneri ndi atumwi; ndipo ena a iwo adzawapha, nadzawazunza;


ndipo anatumiza kapolo wake pa nthawi ya phwando kukanena kwa oitanidwawo, Idzani, chifukwa zonse zakonzeka tsopano.


Yesu anayankha iye, Ine ndalankhula zomveka kwa dziko lapansi; ndinaphunzitsa Ine nthawi zonse m'sunagoge ndi mu Kachisi, kumene amasonkhana Ayuda onse; ndipo mobisika sindinalankhule kanthu.


Koma tsiku lomaliza, lalikululo la chikondwerero, Yesu anaimirira nafuula, ndi kunena, Ngati pali munthu akumva ludzu, adze kwa Ine, namwe.


Ndipo adzalalikira bwanji, ngati satumidwa? Monganso kwalembedwa, Okometsetsa ndithu ali mapazi a iwo akulalikira Uthenga Wabwino wa zinthu zabwino.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa