Miyambo 8:3 - Buku Lopatulika3 pambali pa chipata polowera m'mudzi, polowa anthu pa makomo ifuula: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 pambali pa chipata polowera m'mudzi, polowa anthu pa makomo ifuula: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Imafuula pafupi ndi zipata kumaso kwa mzinda, ndiponso pamakomo poloŵera, imati, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Imafuwula pafupi ndi zipata zolowera mu mzinda, pa makomo olowera imafuwula kuti, Onani mutuwo |