Miyambo 8:2 - Buku Lopatulika2 Iima pamwamba pa mtunda, pa mphambano za makwalala; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Iima pamwamba pa mtunda, pa mphambano za makwalala; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Nzeru imakhala pa zitunda m'mbali mwa njira, imakaima pa mphambano za miseu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Nzeru imayima pa zitunda mʼmbali mwa njira, imayima pa mphambano ya misewu. Onani mutuwo |