Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Miyambo 7:9 - Buku Lopatulika

9 pa madzulo kuli sisiro, pakati pa usiku pali mdima.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 pa madzulo kuli sisiro, pakati pa usiku pali mdima.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Inali nthaŵi ya chisisira, madzulo, nthaŵi yausiku, kuli mdima.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Inali nthawi yachisisira madzulo, nthawi ya usiku, kuli mdima.

Onani mutuwo Koperani




Miyambo 7:9
6 Mawu Ofanana  

Ndipo panali, nthawi yomweyo, iye analowa m'nyumba kuti agwire ntchito yake; ndipo munalibe amuna a m'nyumba m'katimo.


Ndipo mukhale naye chisungire kufikira tsiku lakhumi ndi chinai la mwezi womwe; ndipo gulu lonse la Israele lizamuphe madzulo.


Ndipo taona, mkaziyo anamchingamira, atavala zadama wochenjera mtima,


ndipo musayanjane nazo ntchito za mdima zosabala kanthu, koma makamakanso muzitsutse;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa