Miyambo 7:4 - Buku Lopatulika4 Nena kwa nzeru, Ndiwe mlongo wanga; nutche luntha mbale wako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Nena kwa nzeru, Ndiwe mlongo wanga; nutche luntha mbale wako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Nzeru uiwuze kuti, “Iwe ndiwe mlongo wanga,” ndipo khalidwe la kumvetsa zinthu ulitchule kuti, “Bwenzi langa lapamtima.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Nzeru uyiwuze kuti, “Iwe ndiwe mlongo wanga,” ndipo khalidwe lomvetsa bwino zinthu ulitchule kuti, “Bwenzi langa lapamtima.” Onani mutuwo |