Miyambo 7:18 - Buku Lopatulika18 Tiye tikondwere ndi chikondano mpaka mamawa; tidzisangalatse ndi chiyanjano. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Tiye tikondwere ndi chikondano mpaka mamawa; tidzisangalatse ndi chiyanjano. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Bwera tsono, tikhale malo amodzi mpaka m'maŵa, tisangalatsane ndi chikondi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Bwera, tiye tikhale malo amodzi kukondwerera chikondi mpaka mmawa; tiye tisangalatsane mwachikondi! Onani mutuwo |