Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Miyambo 7:16 - Buku Lopatulika

16 Ndayala zofunda pakama panga, nsalu zamawangamawanga za thonje la ku Ejipito,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Ndayala zofunda pakama panga, nsalu zamawangamawanga za thonje la ku Ejipito,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Pabedi panga ndayalapo zofunda zabwino, pali nsalu zabafuta zamaŵangamaŵanga za ku Ejipito.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Pa bedi panga ndayalapo nsalu zosalala zokongola zochokera ku Igupto.

Onani mutuwo Koperani




Miyambo 7:16
8 Mawu Ofanana  

Ndipo akavalo a Solomoni anachokera ku Ejipito; anthu a malonda a mfumu anawagula magulumagulu, gulu lililonse mtengo wake.


Adzipangira zimbwi zamawangamawanga; navala bafuta ndi guta wofiirira.


Chifukwa chake ndatuluka kudzakuchingamira, kudzafunitsa nkhope yako, ndipo ndakupeza.


Taona, wakongolatu, bwenzi langa, mnyamatawe, inde, wakongoletsa; pogona pathu mpa msipu.


Komanso iwo amene agwira ntchito yakupala thonje, ndi iwo amene aomba nsalu yoyera, adzakhala ndi manyazi.


Thanga lako ndi labafuta wopikapika wa ku Ejipito, likhale ngati mbendera yako; chophimba chako ndicho nsalu yamadzi ndi yofiirira zochokera ku zisumbu za Elisa.


Taona, ndimponya iye pakama, ndi iwo akuchita chigololo naye kuwalonga m'chisautso chachikulu, ngati salapa iwo ndi kuleka ntchito zake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa