Miyambo 6:8 - Buku Lopatulika8 koma zitengeratu zakudya zao m'malimwe; ndipo zituta dzinthu zao m'masika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 koma zitengeratu zakudya zao m'malimwe; nizituta dzinthu zao m'masika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Komabe imakonzeratu chakudya chake m'malimwe, ndipo imatuta chakudyacho m'masika. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 komabe zimasungiratu chakudya chake nthawi ya chilimwe ndipo zimatuta chakudyacho nthawi yokolola. Onani mutuwo |