Miyambo 6:7 - Buku Lopatulika7 zilibe mfumu, ngakhale kapitao, ngakhale mkulu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 zilibe mfumu, ngakhale kapitao, ngakhale mkulu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Ilibe ndi mfumu yomwe, ilibe kapitao kapena wolamulira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Zilibe mfumu, zilibe woyangʼanira kapena wolamulira, Onani mutuwo |