Miyambo 6:3 - Buku Lopatulika3 Chita ichi tsono; mwananga, nudzipulumutse; popeza walowa m'dzanja la mnzako, pita nudzichepetse, numdandaulire mnzako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Chita ichi tsono; mwananga, nudzipulumutse; popeza walowa m'dzanja la mnzako, pita nudzichepetse, numdandaulire mnzako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Ndiye iwe mwana wanga, popeza kuti wadziponya m'manja mwa mnzako, chita izi kuti udzipulumutse: nyamuka, pita msanga, ukampemphe kuti akumasule. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Tsono popeza iwe mwana wanga wadziponya mʼmanja mwa mnansi wako, chita izi kuti udzipulumutse: pita msanga ukamupemphe mnansi wako; kuti akumasule! Onani mutuwo |