Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Miyambo 5:10 - Buku Lopatulika

10 kuti mphamvu yako isakhutitse alendo, ndi kuti usagwire ntchito m'nyumba ya wachilendo;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 kuti mphamvu yako isakhutitse alendo, ndi kuti usagwire ntchito m'nyumba ya wachilendo;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Mwinanso alendo adzadyerera chuma chako, phindu la ntchito zako lidzagwa m'manja mwa munthu wachilendo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 kapenanso alendo angadyerere chuma chako ndi phindu la ntchito yako kulemeretsa anthu ena.

Onani mutuwo Koperani




Miyambo 5:10
8 Mawu Ofanana  

Mwamuna wokonda nzeru akondweretsa atate wake; koma wotsagana ndi akazi adama amwaza chuma.


Musapereke mphamvu yako kwa akazi, ngakhale kuyenda m'njira yoononga mafumu.


ungalire pa chimaliziro chako, pothera nyama yako ndi thupi lako;


kuti ungapereke ulemu wako kwa ena, ndi zaka zako kwa ankhanza;


Pakuti ukayamba ndi mkazi wadama, udzamaliza ndi nyenyeswa; ndipo mkazi wa mwini amasaka moyo wa mtengowapatali.


Sadzalabadira chiombolo chilichonse, sadzapembedzeka ngakhale uchulukitsa malipo.


Alendo anatha mphamvu yake osachidziwa iye; imvi zomwe zampakiza osachidziwa iye.


Koma pamene anadza mwana wanu uyu, wakutha zamoyo zanu ndi akazi achiwerewere, munamphera iye mwanawang'ombe wonenepa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa