Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Miyambo 4:1 - Buku Lopatulika

1 Ananu, mverani mwambo wa atate, nimutchere makutu mukadziwe luntha;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Ananu, mverani mwambo wa atate, nimutchere makutu mukadziwe luntha;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Ana inu, mverani malangizo a atate anu, tcherani khutu, kuti mupate nzeru zodziŵira zinthu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Ananu, mverani malangizo a abambo anu; tcherani khutu kuti mupeze nzeru zodziwira zinthu.

Onani mutuwo Koperani




Miyambo 4:1
15 Mawu Ofanana  

Sonkhanani, tamvani, ana aamuna a Yakobo; tamverani Israele atate wanu.


Idzani ananu ndimvereni ine, ndidzakulangizani zakumuopa Yehova.


Kudziwa nzeru ndi mwambo; kuzindikira mau ozindikiritsa;


Mwananga, tamva mwambo wa atate wako, ndi kusasiya chilangizo cha amai ako;


Mwana wanzeru amamvera mwambo wa atate; koma wonyoza samvera chidzudzulo.


Tamvera uphungu, nulandire mwambo, kuti ukhale wanzeru pa chimaliziro chako.


Tchera makutu ako, numvere mau a anzeru, nulozetse mtima wako kukadziwa zanga.


Mwananga, mvera nzeru yanga; tcherera makutu ku luntha langa;


Nena kwa nzeru, Ndiwe mlongo wanga; nutche luntha mbale wako.


Ndipo ife tamva mau a Yonadabu mwana wa Rekabu kholo lathu m'zonse zimene anatiuza ife, zakuti tisamwe vinyo masiku athu onse, ife, akazi athu, ana athu aamuna ndi aakazi;


Mwa ichi tiyenera kusamaliradi zimene tidazimvazi kuti kapena tingatengedwe ndi kusiyana nazo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa