Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Miyambo 3:4 - Buku Lopatulika

4 motero udzapeza chisomo ndi nzeru yabwino, pamaso pa Mulungu ndi anthu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 motero udzapeza chisomo ndi nzeru yabwino, pamaso pa Mulungu ndi anthu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Choncho udzapeza kuyanja ndi mbiri yabwino pamaso pa Mulungu ndi pa anthunso.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Ukatero udzapeza kuyanja ndi mbiri yabwino pamaso pa Mulungu ndi anthu.

Onani mutuwo Koperani




Miyambo 3:4
14 Mawu Ofanana  

Koma Yehova anali ndi Yosefe namchitira iye zokoma, nampatsa ufulu pamaso pa woyang'anira kaidi.


Kumuopa Yehova ndiko chiyambi cha nzeru; onse akuchita chotero ali nacho chidziwitso chokoma; chilemekezo chake chikhalitsa kosatha.


Yehova akomera mtima munthu wabwino; koma munthu wa ziwembu amtsutsa.


Nzeru yabwino ipatsa chisomo; koma njira ya achiwembu ili makolokoto.


pakuti wondipeza ine apeza moyo; Yehova adzamkomera mtima.


Ndipo Mulungu anamkometsera Daniele mtima wa mkulu wa adindo, amchitire chifundo.


Ndipo Yesu anakulabe m'nzeru ndi mumsinkhu, ndi m'chisomo cha pa Mulungu ndi cha pa anthu.


nalemekeza Mulungu, ndi kukhala nacho chisomo ndi anthu onse. Ndipo Ambuye anawaonjezera tsiku ndi tsiku amene akuti apulumutsidwe.


Pakuti iye amene atumikira Khristu mu izi akondweretsa Mulungu, navomerezeka ndi anthu.


pakuti tikonzeratu zinthu zokoma, si pamaso pa Ambuye pokha, komanso pamaso pa anthu.


Ndipo Yehova anakumbukira Hana, naima iye, nabala ana aamuna atatu, ndi ana aakazi awiri. Ndipo mwanayo Samuele anakula pamaso pa Yehova.


Ndipo mwanayo Samuele anakulakula, ndipo Yehova ndi anthu omwe anamkomera mtima.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa