Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Miyambo 26:3 - Buku Lopatulika

3 Chikoti chiyenera kavalo, ndi cham'kamwa chiyenera bulu, ndi nthyole iyenera pamsana pa zitsiru.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Chikoti chiyenera kavalo, ndi cham'kamwa chiyenera bulu, ndi nthyole iyenera pamsana pa zitsiru.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Mkwapulo ndi wokwapulira kavalo, chitsulo ncha m'kamwa mwa bulu, chonchonso ndodo ndi yoyenerera zitsiru.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Mkwapulo ndi wokwapulira kavalo, chitsulo ndi cha mʼkamwa mwa bulu, choncho ndodo ndi yoyenera ku msana wa chitsiru.

Onani mutuwo Koperani




Miyambo 26:3
10 Mawu Ofanana  

Musakhale monga kavalo, kapena ngati bulu, wopanda nzeru; zomangira zao ndizo cham'kamwa ndi chapamutu zakuwakokera, pakuti ukapanda kutero sadzakuyandikiza.


Nzeru ipezedwa m'milomo ya wozindikira; koma wopusa pamsana pake nthyole.


Chidzudzulo chilowa m'kati mwa wozindikira, kopambana ndi kukwapula wopusa kwambiri.


Menya wonyoza, ndipo achibwana adzachenjera; nudzudzule wozindikira adzazindikira nzeru.


Akonzera onyoza chiweruzo, ndi mikwingwirima pamsana pa opusa.


Ungakhale ukonola chitsiru m'mtondo ndi munsi, pamodzi ndi mphale, koma utsiru wake sudzamchoka.


Kodi ndifike kwa inu ndi ndodo, kapena mwachikondi, ndi mzimu wakufatsa?


ndi kukhala okonzeka kubwezera chilango kusamvera konse, pamene kumvera kwanu kudzakwaniridwa.


Ndinanena kale, ndipo ndinena ndisanafikeko, monga pamene ndinali pomwepo kachiwiri kaja, pokhala ine palibe, kwa iwo adachimwa kale ndi kwa onse otsala, kuti, ngati ndidzanso sindidzawaleka;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa