Miyambo 26:18 - Buku Lopatulika18 Monga woyaluka woponya nsakali, mivi, ndi imfa, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Monga woyaluka woponya nsakali, mivi, ndi imfa, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Monga munthu wopenga amene amangoponya nsakali zamoto, kapena mivi yoopsa, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Monga munthu wamisala amene akuponya sakali zamoto kapena mivi yoopsa, Onani mutuwo |