Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Miyambo 24:4 - Buku Lopatulika

4 Kudziwa kudzaza zipinda zake ndi chuma chonse chofunika cha mtengo wake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Kudziwa kudzaza zipinda zake ndi chuma chonse chofunika cha mtengo wake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Wodziŵa zinthu angathe kudzaza zipinda zake ndi chuma chokondweretsa ndi cha mtengo wapatali.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Munthu wodziwa zinthu angathe kudzaza zipinda zake ndi chuma chamtengowapatali ndiponso chabwino.

Onani mutuwo Koperani




Miyambo 24:4
16 Mawu Ofanana  

Pakuti ana a Israele ndi ana a Levi, azibwera nayo nsembe yokweza yatirigu, ndi yavinyo ndi yamafuta, kuzipinda kuli zipangizo za malo opatulika, ndi ansembe akutumikira, ndi odikira, ndi oimbira; kuti tisasiye nyumba ya Mulungu wathu.


Asema njira pakati pa matanthwe, ndi diso lake liona chilichonse cha mtengo wake.


M'nyumba ya wolungama muli katundu wambiri; koma m'phindu la woipa muli vuto.


Alipo golide ndi ngale zambiri; koma milomo yodziwa ndiyo chokometsera cha mtengo wapatali.


Mokhala wanzeru muli katundu wofunika ndi mafuta; koma wopusa angozimeza.


Mwamuna wanzeru ngwamphamvu; munthu wodziwa ankabe nalimba.


Katundu ndi ulemu zili ndi ine, chuma chosatha ndi chilungamo.


kuti ndionetse chuma akundikonda, chikhale cholowa chao, ndi kudzaza mosungira mwao.


Ndipo Iye anati kwa iwo, Chifukwa chake, mlembi aliyense, wophunzitsidwa mu Ufumu wa Kumwamba, ali wofanana ndi munthu mwini banja, amene atulutsa m'chuma chake zinthu zakale ndi zatsopano.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa