Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Miyambo 2:3 - Buku Lopatulika

3 ukaitananso luntha, ndi kufuulira kuti ukazindikire;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 ukaitananso luntha, ndi kufuulira kuti ukazindikire;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Ndikutitu upemphe mtima wozindikira zinthu, ndi kupemba kuti ukhale womvetsa zinthu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 ngati upempha kuti uzindikire zinthu inde kupempha ndi mtima wonse kuti ukhale womvetsa zinthu,

Onani mutuwo Koperani




Miyambo 2:3
15 Mawu Ofanana  

Chokhachi, Yehova akupatse nzeru ndi luntha, nakulangize za Israele, kuti usunge chilamulo cha Yehova Mulungu wako.


Ine ndine mtumiki wanu, ndizindikiritseni; kuti ndidziwe mboni zanu.


Kufuula kwanga kuyandikire pamaso panu, Yehova; mundizindikiritse monga mwa mau anu.


Mundizindikiritse, ndipo ndidzasunga malamulo anu; ndidzawasamalira ndi mtima wanga wonse.


Manja anu anandilenga nandiumba; mundizindikiritse, kuti ndiphunzire malemba anu.


kutcherera makutu ako kunzeru, kulozetsa mtima wako kukuzindikira;


ukaifunafuna ngati siliva, ndi kuipwaira ngati chuma chobisika;


umlemekeze m'njira zako zonse, ndipo Iye adzaongola mayendedwe ako.


Ananu, mverani mwambo wa atate, nimutchere makutu mukadziwe luntha;


Akundikonda ndiwakonda; akundifunafuna adzandipeza.


Potero, ngati inu, okhala oipa, mudziwa kupatsa ana anu mphatso zabwino, koposa kotani nanga Atate wanu wa Kumwamba adzapatsa Mzimu Woyera kwa iwo akumpempha Iye?


Koma wina wa inu ikamsowa nzeru, apemphe kwa Mulungu, amene apatsa kwa onse modzala manja, niwosatonza; ndipo adzampatsa iye.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa