Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Miyambo 1:9 - Buku Lopatulika

9 pakuti izi ndi korona wa chisomo pamutu pako, ndi mkanda pakhosi pako.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 pakuti izi ndi korona wa chisomo pamtu pako, ndi mkanda pakhosi pako.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Zili ngati nsangamutu yokongola yamaluŵa pamutu pako, zili ngati mkanda wa m'khosi mwako.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Ali ngati sangamutu yokongola ya maluwa pamutu pako ndiponso ali ngati mkanda mʼkhosi mwako.

Onani mutuwo Koperani




Miyambo 1:9
16 Mawu Ofanana  

Ndipo Farao anachotsa mphete yosindikizira yake padzanja lake, naiveka padzanja la Yosefe, namveka iye ndi zovalira zabafuta, naika unyolo wagolide pakhosi pake;


Chifukwa chake kudzikuza kunga unyolo pakhosi pao; achivala chiwawa ngati malaya.


ndipo mtima wako udzatengapo moyo, ndi khosi lako chisomo.


Chifundo ndi choonadi zisakusiye; uzimange pakhosi pako; uzilembe pamtima pako;


Idzaika chisada cha chisomo pamutu pako; idzakupatsa korona wokongola.


Masaya ako akongola ndi nkhata zatsitsi, ndi khosi lako ndi zinganga za mkanda wonyezimira.


Walanda mtima wanga, mlongo wanga, mkwatibwi; walanda mtima wanga ndi diso lako limodzi, ndi chinganga chimodzi cha pakhosi pako.


mbera, ndi makoza, ndi nsalu za pankhope;


Ndipo ife tamva mau a Yonadabu mwana wa Rekabu kholo lathu m'zonse zimene anatiuza ife, zakuti tisamwe vinyo masiku athu onse, ife, akazi athu, ana athu aamuna ndi aakazi;


Ndinakukometseranso ndi zokometsera, ndi kuika zigwinjiri m'manja mwako, ndi unyolo m'khosi mwako.


Koma ndamva ine za iwe, kuti ukhoza kutanthauzira mau, ndi kumasula mfundo; tsono ukakhoza kuwerenga lembalo, ndi kundidziwitsa kumasulira kwake, udzavekedwa chibakuwa, ndi unyolo wagolide m'khosi mwako; nudzakhala wolamulira wachitatu mu ufumuwo.


Pamenepo Belisazara analamulira, ndipo anaveka Daniele chibakuwa, ndi unyolo wagolide m'khosi mwake, nalalikira za iye kuti ndiye wolamulira wachitatu mu ufumumo.


Nifuulitsa mfumu abwere nao openda, Ababiloni, ndi alauli. Mfumu inalankhula, niti kwa anzeru a ku Babiloni, Aliyense amene adzawerenga lemba ili, nadzandifotokozera kumasulira kwake, adzavekedwa chibakuwa, ndi unyolo wagolide m'khosi mwake, nadzakhala wolamulira wachitatu mu ufumuwu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa